70 episodes

Kufalitsa uthenga wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

Chuma mzikho zadothi John Joseph Matandika

    • Religion & Spirituality

Kufalitsa uthenga wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

    Nkhondo ya Uzimu

    Nkhondo ya Uzimu

    The LORD God said to the serpent, “Because you have done this, cursed are you above all livestock and above all beasts of the field; on your belly you shall go, and dust you shall eat all the days of your life. I will put enmity between you and the woman, and between your offspring and her offspring; he shall bruise your head, and you shall bruise his heel.”

    (Gen 3:14-15)

    • 29 min
    Mtengo wa Chiyero

    Mtengo wa Chiyero

    Ngati munthu adza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale ake, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Ndipo amene ali yense sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Pakuti ndani wa inu amene akufuna kumanga nsanja yayitali, sayamba wakhala pansi, nawerengera mtengo wake, awone ngati ali nazo zakuyimaliza? Kuti kungachitike, pamene atakhazika pansi miyala ya maziko ake, wosakhoza kuyimaliza, anthu onse woyang’ana adzayamba kumseka iye. Ndikunena kuti, Munthu uyu adayamba kumanga, koma sadathe kumaliza. Kapena mfumu yanji pakupita kukomana ndi nkhondo ya mfumu imzake, siyiyamba yakhala pansi, nafunsana ndi akulu ngati akhoza ndi asilikari ake zikwi khumi kulimbana naye wina uja alikudza kukomana naye ndi asilikari zikwi makumi awiri? Koma ngati sakhoza, atumiza akazembe, pokhala winayo ali kutalitali, nafunsa za mtendere. Chomwecho ndinena kwa inu, yense wa inu amene sakaniza zonse ali nazo, sakhoza kukhala wophunzira wanga.

    (Luk 14:26-33)

    • 27 min
    Kusamvetsetsa Chiyero Gawo 1

    Kusamvetsetsa Chiyero Gawo 1

    Ndipo wophunzira a Yohane ndi Afarisi adalimkusala kudya; ndipo anadza, nanena ndi Iye, Bwanji asala kudya wophunzira a Yohane, ndi wophunzira Afarisi, koma wophunzira anu sasala kudya? Ndipo Yesu adanena nawo, Kodi akhoza kusala kudya ana a ukwati pamene mkwati ali pamodzi nawo? Pokhala ali naye mkwati pamodzi ndi iwo sakhoza kusala. Koma adzafika masiku, pamene mkwati adzachotsedwa kwa iwo, ndipo pamenepo adzasala kudya m`masiku amenewo. Palibe munthu asokerera chigamba cha nsalu yatsopano pa chobvala chakale; mwina chigamba chatsopanocho chikhoza kuzomoka kuyakaleyo, ndipo chibowo chake chikhala chachikulu. Ndipo palibe munthu amathira vinyo watsopano m’mabotolo akale; pena vinyo adzaswa mabotolo, ndipo akhoza kuwonongeka vinyo, ndi mabotolo omwe; koma vinyo watsopano, amathiridwa m’mabotolo atsopano.

    (Mar 2:18-22)

    • 25 min
    Kulungamitsidwa Mutu 2

    Kulungamitsidwa Mutu 2

    Monga kwalembedwa, palibe m’modzi wolungama, inde palibe m’modzi; Palibe m’modzi wakudziwitsa, palibe m’modzi wakufunafuna Mulungu; Onsewa apatuka njira, wonsewa pamodzi akhala wopanda phindu; palibe m’modzi wochita zabwino, inde, palibe m’modzi ndithu. M’mero mwawo muli manda apululu; Ndi lilime lawo amanyenga; ululu wa njoka uli pansi pa milomo yawo; M’kamwa mwawo mudzala ndi zotemberera ndi zowawa; Miyendo yawo ichita liwiro kukhetsa mwazi; Kusakaza ndi kusawuka kuli m’njira zawo; Ndipo njira ya mtendere sadayidziwa; Kumuopa Mulungu kulibe pamaso pawo. Ndipo tidziwa kuti zinthu zili zonse chizinena chilamulo zichiyankhulira iwo ali pansi pa chilamulo; kuti pakamwa ponse patsekedwe, ndi dziko lonse lapansi likatsutsidwe pamaso pa Mulungu. Chifukwa chake pamaso pake palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi ntchito za lamulo; pakuti uchimo udziwika ndi lamulo.

    (Rom 3:10-20)

    • 26 min
    Thandizo

    Thandizo

    Koma pamene wafika Nkhoswe, amene Ine ndidzamtuma kwa inu kuchokera kwa Atate, ndiye Mzimu wa chowonadi amene atuluka kwa Atate, Iyeyu adzandichitira Ine umboni. Ndipo inunso mudzachitira umboni, chifukwa mudali ndi Ine kuyambira pachiyambi.

    (Joh 15:26-27)

    • 25 min
    Kuyeretsedwa Mutu 1

    Kuyeretsedwa Mutu 1

    Chifukwa chake ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera. Ndipo musafanizidwe ndi makhalidwe apansi pano; koma mukhale wosandulika, mwa kukonzanso kwa mtima wanu, kuti mukazindikire chimene chiri chifuno cha Mulungu, chabwino, ndi cholandirika ndi changwiro.

    (Rom 12:1-2)

    • 29 min

Top Podcasts In Religion & Spirituality

Santo Rosario
RadioSeminario
Astrology of the Week Ahead with Chani Nicholas
CHANI
These Are The Days
Jeremy + Audrey Roloff
The Bible in a Year (with Fr. Mike Schmitz)
Ascension
Yasir Qadhi
Muslim Central
HungryGen
HungryGen